Wotamba akumana ndi wastaniki- The story of El Mind and Slessor

Ndewu ya Njobvu timavutika ndife nyelele. Zili ngati bullets kukumana ndi noma. Kodi pakati pa chibwente ndi kanyenya mungasankhe chani? Nanga chitumbuwa ndi chigumu? Pakati pa itel ndi Astro deal ndi cha? Nike ndi Adidas mungakwele iti? Lilongwe ndi Blantyre malo koma ati? Kodi abale, mayankho a izi ndiovuta kusankha ngati Slessor akakumana ndi El mind !!!! Titsani nyimbo imeneyi ndipo musankhe!

Comments

You might also like